Ezara 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa ana a Pinihasi+ panali Gerisomu, pa ana a Itamara+ panali Danieli, pa ana a Davide panali Hatusi.
2 Pa ana a Pinihasi+ panali Gerisomu, pa ana a Itamara+ panali Danieli, pa ana a Davide panali Hatusi.