Ezara 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa ana a Zatu+ panali Sekaniya mwana wa Yahazieli. Iye anali ndi amuna 300.