Ezara 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa ana a Elamu+ panali Yesaiya mwana wa Ataliya. Iye anali ndi amuna 70.