Ezara 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa ana a Sefatiya+ panali Zebadiya mwana wa Mikayeli. Iye anali ndi amuna 80.