Ezara 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndinawasonkhanitsa pamtsinje umene umafika ku Ahava+ ndipo tinamanga msasa pamenepo nʼkukhalapo masiku atatu. Koma nditafufuza bwinobwino anthuwo komanso ansembe, sindinapezepo Alevi.
15 Ndinawasonkhanitsa pamtsinje umene umafika ku Ahava+ ndipo tinamanga msasa pamenepo nʼkukhalapo masiku atatu. Koma nditafufuza bwinobwino anthuwo komanso ansembe, sindinapezepo Alevi.