Ezara 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako ndinawalamula kuti apite kwa Ido yemwe anali mtsogoleri pamalo otchedwa Kasifiya. Ndinawauza mawu oti akauze Ido ndi abale ake, atumiki apakachisi* omwe anali ku Kasifiyako kuti atibweretsere atumiki apanyumba ya Mulungu wathu.
17 Kenako ndinawalamula kuti apite kwa Ido yemwe anali mtsogoleri pamalo otchedwa Kasifiya. Ndinawauza mawu oti akauze Ido ndi abale ake, atumiki apakachisi* omwe anali ku Kasifiyako kuti atibweretsere atumiki apanyumba ya Mulungu wathu.