Ezara 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano ndaika padera anthu 12 kuchokera pa atsogoleri a ansembe. Mayina awo ndi Serebiya komanso Hasabiya+ pamodzi ndi abale awo 10.
24 Tsopano ndaika padera anthu 12 kuchokera pa atsogoleri a ansembe. Mayina awo ndi Serebiya komanso Hasabiya+ pamodzi ndi abale awo 10.