Ezara 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 mbale 20 zingʼonozingʼono zagolide zolowa zokwana madariki* 1,000 ndi ziwiya ziwiri zamkuwa wabwino wonyezimira mofiirira, zamtengo wapatali ngati golide. Ezara Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), ptsa. 2141-2142, 2242
27 mbale 20 zingʼonozingʼono zagolide zolowa zokwana madariki* 1,000 ndi ziwiya ziwiri zamkuwa wabwino wonyezimira mofiirira, zamtengo wapatali ngati golide.