Ezara 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kenako ndinawauza kuti: “Inu ndinu oyera kwa Yehova.+ Ziwiyazi ndi zopatulika ndipo siliva komanso golideyu ndi nsembe yaufulu yopita kwa Yehova Mulungu wa makolo anu.
28 Kenako ndinawauza kuti: “Inu ndinu oyera kwa Yehova.+ Ziwiyazi ndi zopatulika ndipo siliva komanso golideyu ndi nsembe yaufulu yopita kwa Yehova Mulungu wa makolo anu.