Ezara 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako tinachoka pamtsinje wa Ahava+ pa tsiku la 12 la mwezi woyamba+ kupita ku Yerusalemu. Dzanja la Mulungu wathu linkatithandiza pa ulendowu moti anatipulumutsa kwa adani ndiponso achifwamba mʼnjira.
31 Kenako tinachoka pamtsinje wa Ahava+ pa tsiku la 12 la mwezi woyamba+ kupita ku Yerusalemu. Dzanja la Mulungu wathu linkatithandiza pa ulendowu moti anatipulumutsa kwa adani ndiponso achifwamba mʼnjira.