Ezara 8:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kenako tinapereka malamulo a mfumu+ kwa masatarapi* a mfumu ndi abwanamkubwa a kutsidya lina la Mtsinje.*+ Malamulowo anathandiza anthuwo ndiponso anathandiza panyumba ya Mulungu woona.+
36 Kenako tinapereka malamulo a mfumu+ kwa masatarapi* a mfumu ndi abwanamkubwa a kutsidya lina la Mtsinje.*+ Malamulowo anathandiza anthuwo ndiponso anathandiza panyumba ya Mulungu woona.+