-
Ezara 9:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Nditangomva nkhaniyi, ndinangʼamba zovala zanga nʼkuzula tsitsi langa ndi ndevu zanga, ndipo ndinakhala pansi nditakhumudwa kwambiri.
-