4 Aliyense amene ankalemekeza mawu a Mulungu wa Isiraeli anabwera nʼkundizungulira chifukwa cha kusakhulupirika kwa anthu amene anachokera ku ukapolo. Pa nthawiyi nʼkuti ndili wokhumudwa kwambiri ndipo ndinakhala pansi mpaka nthawi yopereka nsembe yambewu yamadzulo.+