Ezara 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi yopereka nsembe yambewu yamadzulo,+ ndinaimirira mwamanyazi, zovala zanga zili zongʼambika ndipo ndinagwada nʼkukweza manja anga kwa Yehova Mulungu wanga.
5 Pa nthawi yopereka nsembe yambewu yamadzulo,+ ndinaimirira mwamanyazi, zovala zanga zili zongʼambika ndipo ndinagwada nʼkukweza manja anga kwa Yehova Mulungu wanga.