-
Ezara 9:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Choncho musakapereke ana anu aakazi kwa ana awo aamuna, kapena kutenga ana awo aakazi nʼkuwapereka kwa ana anu aamuna.+ Musakalole kuti akhale pamtendere ndiponso kuti atukuke.+ Mukachite zimenezi kuti mukakhale amphamvu, mukadye zabwino zamʼdzikolo ndiponso kuti mukalitenge kuti likhale la ana anu mpaka kalekale.’
-