Nehemiya 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndinati: “Inu Yehova Mulungu wakumwamba, Mulungu wamkulu komanso wochititsa mantha. Inu mumakwaniritsa pangano lanu ndipo mumasonyeza chikondi chokhulupirika kwa anthu amene amakukondani ndi kusunga malamulo anu.+
5 Ndinati: “Inu Yehova Mulungu wakumwamba, Mulungu wamkulu komanso wochititsa mantha. Inu mumakwaniritsa pangano lanu ndipo mumasonyeza chikondi chokhulupirika kwa anthu amene amakukondani ndi kusunga malamulo anu.+