Nehemiya 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tachita zinthu zolakwika pamaso panu+ ndipo sitinasunge malamulo, malangizo ndi ziweruzo zimene munapatsa mtumiki wanu Mose.+
7 Tachita zinthu zolakwika pamaso panu+ ndipo sitinasunge malamulo, malangizo ndi ziweruzo zimene munapatsa mtumiki wanu Mose.+