Nehemiya 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mʼmwezi wa Nisani,* mʼchaka cha 20+ cha mfumu Aritasasita,+ mfumuyo inkafuna vinyo choncho ndinatenga vinyoyo nʼkukapereka kwa mfumu ngati mmene ndinkachitira nthawi zonse.+ Koma ndinali ndisanakhalepo wachisoni pamaso pake. Nehemiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:1 Nsanja ya Olonda,2/1/2006, ptsa. 8-910/15/1990, ptsa. 10-111/15/1986, tsa. 7 Ulosi wa Danieli, tsa. 197
2 Mʼmwezi wa Nisani,* mʼchaka cha 20+ cha mfumu Aritasasita,+ mfumuyo inkafuna vinyo choncho ndinatenga vinyoyo nʼkukapereka kwa mfumu ngati mmene ndinkachitira nthawi zonse.+ Koma ndinali ndisanakhalepo wachisoni pamaso pake.
2:1 Nsanja ya Olonda,2/1/2006, ptsa. 8-910/15/1990, ptsa. 10-111/15/1986, tsa. 7 Ulosi wa Danieli, tsa. 197