-
Nehemiya 2:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Choncho mfumu inati: “Nʼchifukwa chiyani ukuoneka wachisoni pamene sukudwala? Payenera kuti pali chinachake chimene chikukuvutitsa mumtima.” Atanena zimenezi ndinachita mantha kwambiri.
-