Nehemiya 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mfumuyo inandifunsa kuti: “Ndiye ukufuna chiyani?” Nthawi yomweyo ndinapemphera kwa Mulungu wakumwamba.+ Nehemiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:4 Nsanja ya Olonda,7/15/1987, tsa. 122/15/1986, tsa. 25
4 Mfumuyo inandifunsa kuti: “Ndiye ukufuna chiyani?” Nthawi yomweyo ndinapemphera kwa Mulungu wakumwamba.+