Nehemiya 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako ndinauza mfumu kuti: “Ngati zili bwino ndi inu mfumu, ndipo ngati mungandikomere mtima ine mtumiki wanu, munditumize ku Yuda, kumzinda umene makolo anga anaikidwako kuti ndikaumangenso.”+
5 Kenako ndinauza mfumu kuti: “Ngati zili bwino ndi inu mfumu, ndipo ngati mungandikomere mtima ine mtumiki wanu, munditumize ku Yuda, kumzinda umene makolo anga anaikidwako kuti ndikaumangenso.”+