Nehemiya 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Sanibalati wa ku Beti-horoni+ ndi Tobia,+ mtumiki wa Chiamoni,+ anakwiya kwambiri atamva zimenezi komanso ataona kuti kwabwera munthu wodzachitira Aisiraeli zinthu zabwino.
10 Sanibalati wa ku Beti-horoni+ ndi Tobia,+ mtumiki wa Chiamoni,+ anakwiya kwambiri atamva zimenezi komanso ataona kuti kwabwera munthu wodzachitira Aisiraeli zinthu zabwino.