-
Nehemiya 2:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndinadzuka usiku limodzi ndi amuna angapo amene ndinali nawo. Sindinauze aliyense zimene Mulungu wanga anaika mumtima mwanga zoti ndichitire Yerusalemu. Pa nthawiyo ndinalibe chiweto chilichonse kupatulapo chiweto chimene ndinakwerapo.
-