Nehemiya 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Atsogoleri+ sanadziwe kumene ndinapita komanso zomwe ndinkachita chifukwa sindinanene chilichonse kwa Ayuda, ansembe, anthu olemekezeka, atsogoleri ndi anthu ena onse ogwira ntchito.
16 Atsogoleri+ sanadziwe kumene ndinapita komanso zomwe ndinkachita chifukwa sindinanene chilichonse kwa Ayuda, ansembe, anthu olemekezeka, atsogoleri ndi anthu ena onse ogwira ntchito.