Nehemiya 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndinawauzanso mmene dzanja la Mulungu wanga landithandizira+ ndiponso mawu amene mfumu inandiuza.+ Pamenepo iwo anati: “Tiyeni timange mpandawo.” Choncho anadzilimbitsa* kuti agwire ntchito yabwinoyi.+
18 Ndinawauzanso mmene dzanja la Mulungu wanga landithandizira+ ndiponso mawu amene mfumu inandiuza.+ Pamenepo iwo anati: “Tiyeni timange mpandawo.” Choncho anadzilimbitsa* kuti agwire ntchito yabwinoyi.+