Nehemiya 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Sanibalati wa ku Beti-horoni, Tobia+ mtumiki wa Chiamoni+ ndi Gesemu Mluya+ atamva zimenezi anayamba kutiseka ndi kutinyoza.+ Iwo anati: “Nʼchiyani chimene mukuchitachi? Kodi mukugalukira mfumu?”+
19 Ndiyeno Sanibalati wa ku Beti-horoni, Tobia+ mtumiki wa Chiamoni+ ndi Gesemu Mluya+ atamva zimenezi anayamba kutiseka ndi kutinyoza.+ Iwo anati: “Nʼchiyani chimene mukuchitachi? Kodi mukugalukira mfumu?”+