Nehemiya 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ana a Haseneya anamanga Geti la Nsomba.+ Iwo analipangira felemu lamatabwa+ nʼkuika zitseko, anamphatika ndi mipiringidzo.
3 Ana a Haseneya anamanga Geti la Nsomba.+ Iwo analipangira felemu lamatabwa+ nʼkuika zitseko, anamphatika ndi mipiringidzo.