Nehemiya 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Malikiya mwana wa Rekabu, kalonga wa chigawo cha Beti-hakeremu,+ anakonza Geti la Milu ya Phulusa. Analikonza nʼkuika zitseko, anamphatika ndi mipiringidzo. Nehemiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:14 Yeremiya, ptsa. 159-160
14 Malikiya mwana wa Rekabu, kalonga wa chigawo cha Beti-hakeremu,+ anakonza Geti la Milu ya Phulusa. Analikonza nʼkuika zitseko, anamphatika ndi mipiringidzo.