Nehemiya 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Alevi, moyangʼaniridwa ndi Rehumu mwana wa Bani, anakonza mpandawo kuchokera pamene Nehemiya analekezera. Hasabiya, kalonga wa hafu ya chigawo cha Keila,+ anakonza mpandawo mʼchigawo chake kuchokera pamene Alevi analekezera.
17 Alevi, moyangʼaniridwa ndi Rehumu mwana wa Bani, anakonza mpandawo kuchokera pamene Nehemiya analekezera. Hasabiya, kalonga wa hafu ya chigawo cha Keila,+ anakonza mpandawo mʼchigawo chake kuchokera pamene Alevi analekezera.