-
Nehemiya 3:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Kuchokera pamenepo, abale awo anakonza mpandawo moyangʼaniridwa ndi Bavai mwana wa Henadadi, kalonga wa hafu ya chigawo cha Keila.
-