Nehemiya 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Meremoti+ mwana wa Uliya, mwana wa Hakozi, anakonza gawo lina la mpandawo kuchokera pageti la nyumba ya Eliyasibu mpaka pamene nyumbayo inathera.
21 Meremoti+ mwana wa Uliya, mwana wa Hakozi, anakonza gawo lina la mpandawo kuchokera pageti la nyumba ya Eliyasibu mpaka pamene nyumbayo inathera.