Nehemiya 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Atumiki apakachisi*+ omwe ankakhala ku Ofeli+ anakonza mpandawo mpaka patsogolo pa Geti la Kumadzi,+ kumʼmawa. Iwo anakonzanso nsanja yomwe inatulukira kunja kwa mpanda.
26 Atumiki apakachisi*+ omwe ankakhala ku Ofeli+ anakonza mpandawo mpaka patsogolo pa Geti la Kumadzi,+ kumʼmawa. Iwo anakonzanso nsanja yomwe inatulukira kunja kwa mpanda.