Nehemiya 3:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Hananiya mwana wa Selemiya ndi Hanuni mwana wa 6 wa Zalafi, anakonzanso chigawo china cha mpanda. Mesulamu+ mwana wa Berekiya, anakonza mpandawo kutsogolo kwa nyumba yake kuchokera pamene Hananiya analekezera.
30 Hananiya mwana wa Selemiya ndi Hanuni mwana wa 6 wa Zalafi, anakonzanso chigawo china cha mpanda. Mesulamu+ mwana wa Berekiya, anakonza mpandawo kutsogolo kwa nyumba yake kuchokera pamene Hananiya analekezera.