Nehemiya 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Sanibalati+ atangomva kuti tikumanganso mpanda, anakwiya ndiponso anapsa mtima kwambiri moti anapitiriza kunyoza Ayuda.
4 Sanibalati+ atangomva kuti tikumanganso mpanda, anakwiya ndiponso anapsa mtima kwambiri moti anapitiriza kunyoza Ayuda.