Nehemiya 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nehemiya anati: “Inu Mulungu wathu, onani mmene akutinyozera.+ Abwezereni chipongwe chawo+ ndipo lolani kuti atengedwe ngati katundu kupita ku ukapolo.
4 Nehemiya anati: “Inu Mulungu wathu, onani mmene akutinyozera.+ Abwezereni chipongwe chawo+ ndipo lolani kuti atengedwe ngati katundu kupita ku ukapolo.