-
Nehemiya 4:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Choncho tinapitiriza kumanga mpandawo moti khoma lonse linalumikizana ndipo linafika hafu kupita mʼmwamba. Anthu anapitiriza kugwira ntchitoyo ndi mtima wonse.
-