Nehemiya 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Sanibalati, Tobia,+ Aluya,+ Aamoni ndi Aasidodi+ atamva kuti ntchito yokonza mpanda wa Yerusalemu ikuyenda bwino ndipo malo ogumuka ayamba kutsekedwa, anakwiya kwambiri.
7 Sanibalati, Tobia,+ Aluya,+ Aamoni ndi Aasidodi+ atamva kuti ntchito yokonza mpanda wa Yerusalemu ikuyenda bwino ndipo malo ogumuka ayamba kutsekedwa, anakwiya kwambiri.