-
Nehemiya 4:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Adani athuwo atamva zoti tadziwa za chiwembu chawo ndipo Mulungu woona wasokoneza mapulani awo, tonse tinayambiranso kumanga mpanda.
-