-
Nehemiya 5:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Komatu ife ndi anzathuwo ndife pachibale ndipo ana athu nʼchimodzimodzi ndi ana awo, koma ife tikufunika kusandutsa ana athu aamuna ndi aakazi kukhala akapolo. Ndipo ana athu ena aakazi tawasandutsa kale akapolo.+ Tilibe mphamvu zoti nʼkuletsa zimenezi chifukwa minda yathu ya tirigu ndi ya mpesa ili mʼmanja mwa anthu ena.”
-