7 Choncho ndinayamba kuganizira zimenezi mumtima mwanga ndipo ndinapeza kuti anthu olemekezeka ndi atsogoleri anali olakwa. Ndiyeno ndinawauza kuti: “Nonsenu mukuumiriza abale anu kuti akupatseni chiwongoladzanja.”+
Komanso ndinaitanitsa msonkhano waukulu chifukwa cha iwowa.