Nehemiya 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo ndinawauza kuti: “Ife tayesetsa kuwombola abale athu a Chiyuda amene anagulitsidwa kwa anthu a mitundu ina. Ndiye inu mukugulitsa abale anu+ ndipo mufuna kuti ife tiwawombole?” Atamva zimenezi anangokhala chete, kusowa chonena.
8 Ndipo ndinawauza kuti: “Ife tayesetsa kuwombola abale athu a Chiyuda amene anagulitsidwa kwa anthu a mitundu ina. Ndiye inu mukugulitsa abale anu+ ndipo mufuna kuti ife tiwawombole?” Atamva zimenezi anangokhala chete, kusowa chonena.