Nehemiya 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiponso ine, abale anga ndi atumiki anga, tikuwakongoza abale athu ndalama ndi chakudya. Chonde, tiyeni tisiye kulandira chiwongoladzanja tikakongoza zinthu.+
10 Ndiponso ine, abale anga ndi atumiki anga, tikuwakongoza abale athu ndalama ndi chakudya. Chonde, tiyeni tisiye kulandira chiwongoladzanja tikakongoza zinthu.+