Nehemiya 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Abwanamkubwa amene analipo ine ndisanakhale, ankalemetsa anthu ndipo tsiku lililonse ankalandira masekeli* 40 asiliva ogulira chakudya ndi vinyo. Komanso atumiki awo ankapondereza anthu. Koma ine sindinachite zimenezo+ chifukwa choopa Mulungu.+
15 Abwanamkubwa amene analipo ine ndisanakhale, ankalemetsa anthu ndipo tsiku lililonse ankalandira masekeli* 40 asiliva ogulira chakudya ndi vinyo. Komanso atumiki awo ankapondereza anthu. Koma ine sindinachite zimenezo+ chifukwa choopa Mulungu.+