Nehemiya 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Sanibalati,+ Tobia, Gesemu Muluya+ komanso adani athu onse atangouzidwa kuti ndamanganso mpanda,+ ndipo ndatseka mipata yonse (ngakhale kuti pa nthawiyo ndinali ndisanaike zitseko mʼmageti),+
6 Ndiyeno Sanibalati,+ Tobia, Gesemu Muluya+ komanso adani athu onse atangouzidwa kuti ndamanganso mpanda,+ ndipo ndatseka mipata yonse (ngakhale kuti pa nthawiyo ndinali ndisanaike zitseko mʼmageti),+