Nehemiya 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 nthawi yomweyo Sanibalati ndi Gesemu ananditumizira uthenga wakuti: “Bwera tidzapangane nthawi yoti tikakumane mʼmudzi wina mʼchigwa cha Ono.”+ Koma ankandikonzera chiwembu. Nehemiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:2 Nsanja ya Olonda,7/1/2007, tsa. 30
2 nthawi yomweyo Sanibalati ndi Gesemu ananditumizira uthenga wakuti: “Bwera tidzapangane nthawi yoti tikakumane mʼmudzi wina mʼchigwa cha Ono.”+ Koma ankandikonzera chiwembu.