-
Nehemiya 6:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kenako Sanibalati ananditumizira uthenga womwewo ulendo wa 5 kudzera mwa mtumiki wake. Mtumikiyo anali ndi kalata yosatseka mʼmanja mwake.
-