Nehemiya 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Onsewo ankangofuna kutichititsa mantha, ndipo ankanena kuti: “Manja awo afooka ndipo asiya kugwira ntchitoyi, moti siitha.”+ Inu Mulungu wanga, limbitsani manja anga.+
9 Onsewo ankangofuna kutichititsa mantha, ndipo ankanena kuti: “Manja awo afooka ndipo asiya kugwira ntchitoyi, moti siitha.”+ Inu Mulungu wanga, limbitsani manja anga.+