-
Nehemiya 6:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Iwo anamulemba ganyu kuti andiopseze komanso kuti ndichite tchimo nʼcholinga choti apeze zifukwa zondiipitsira mbiri kuti azindinyoza.
-