Nehemiya 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu Mulungu wanga, kumbukirani Tobia+ ndi Sanibalati komanso zimene anachitazi. Mukumbukirenso Nowadiya mneneri wamkazi ndi aneneri onse amene ankafuna kundiopseza.
14 Inu Mulungu wanga, kumbukirani Tobia+ ndi Sanibalati komanso zimene anachitazi. Mukumbukirenso Nowadiya mneneri wamkazi ndi aneneri onse amene ankafuna kundiopseza.