Nehemiya 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Adani athu onse atangomva zimenezi komanso anthu a mitundu ina yotizungulira ataona, anachita manyazi kwambiri+ ndipo anazindikira kuti ntchitoyi yatheka chifukwa cha Mulungu wathu.
16 Adani athu onse atangomva zimenezi komanso anthu a mitundu ina yotizungulira ataona, anachita manyazi kwambiri+ ndipo anazindikira kuti ntchitoyi yatheka chifukwa cha Mulungu wathu.